Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Rute 2:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mpongozi wace ananena naye, Unakatola kuti khunkha lero? ndi nchito udaigwira kuti? Adalitsike iye amene anakusamalira. Ndipo anamfotokozera mpongozi wace munthu amene anakagwirako nchito, nati, Dzina lace la munthuyo ndinakagwirako nchito lero ndiye Boazi.

Werengani mutu wathunthu Rute 2

Onani Rute 2:19 nkhani