Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Rute 2:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Boazi anayankha nanena naye, Anandifotokozera bwino zonse unacitira mpongozi wako atafa mwamuna wako; ndi kuti wasiya atate wako ndi mako, ndi dziko lobadwirako iwe, ndi kudza kwa anthu osawadziwa iwe kale.

Werengani mutu wathunthu Rute 2

Onani Rute 2:11 nkhani