Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Rute 1:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Dzina la munthuyo ndiye Elimeleki, ndi dzina la mkazi wace ndiye Naomi, ndi maina a ana ace awiri ndiwo Maloni, ndi Kilioni; ndiwo a ku Efrata ku Betelelehemu-Yuda. Iwowa ndipo analowa m'dziko la Moabu, nakhala komweko.

Werengani mutu wathunthu Rute 1

Onani Rute 1:2 nkhani