Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Rute 1:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nakweza iwo mau ao, naliranso misozi; ndi Olipa anampsompsona mpongozi wace, koma Rute anamkangamira.

Werengani mutu wathunthu Rute 1

Onani Rute 1:14 nkhani