Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 9:54 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anaitana msanga mnyamata wace wosenza zida zace, nanena naye, Solola lupanga lako nundiphe, angamanenere anthu, ndi kuti, Anamupha ndi mkazi. Nampyoza mnyamata wace, nafa iye.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:54 nkhani