Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 4:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yaeli anaturuka kukomana ndi Sisera, nanena naye, Pambuka, mbuye wanga, pambukira kwa ine kuno; usaope. Ndipo anapambukira kwa iye kulowa m'hema, nampfunda ndi cimbwi.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 4

Onani Oweruza 4:18 nkhani