Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 17:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo ku mapiri a Efraimu kunali munthu dzina lace ndiye Mika.

2. Ndipo iye anati kwa amai wace, Ndarama zija mazana khumi ndi limodzi anakuberani zimene munatembererapo, ndi kunenanso m'makutu mwanga, taonani ndaramazo ndiri nazo, ndinazitenga ndine. Pamenepo amai wace anati, Yehova adalitse mwana wanga.

3. Nabwezera amace ndarama zija mazana khumi ndi limodzi; nati amai wace, Kupatula ndapatulira Yehova ndaramazo zicoke ku dzanja langa, zimuke kwa mwana wanga, kupanga nazo dikupempha fano losema ndi fane loyenga; m'mwemo ndikubwezera izi.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 17