Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 17:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nabwezera amace ndarama zija mazana khumi ndi limodzi; nati amai wace, Kupatula ndapatulira Yehova ndaramazo zicoke ku dzanja langa, zimuke kwa mwana wanga, kupanga nazo dikupempha fano losema ndi fane loyenga; m'mwemo ndikubwezera izi.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 17

Onani Oweruza 17:3 nkhani