Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 14:19-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Ndipo mzimu wa Yehova unamgwera Samsoni, natsikira iye kwa Asikeloni, nawakantha amuna makumi atatu, natenga zobvala zao, nawapatsa okumika mwambiwo zobvala zosinthanitsa. Koma adapsa mtima, nakwera kumka ku nyumba ya atate wace.

20. Ndipo mkazi wace wa Samsoni anakhala wa mnzace, amene adakhala bwenzi lace.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 14