Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 1:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anati Adoni-bezeki, Mafumu makumi asanu ndi awiri odulidwa zala zazikuru za m'manja ndi m'mapazi anaola kakudya kao pansi pa gome panga; monga ndinacita ine, momwemo Mulungu wandibwezera. Ndipo anadza naye ku Yerusalemu, nafa iye komweko.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 1

Onani Oweruza 1:7 nkhani