Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 1:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nafitali sanaingitsa nzika za ku Beti-semesi, kapena nzika za ku Beri-anati; koma anakhala pakati pa Akanani, nzika za kudziko; koma nzika za ku Beti-semesi, ndi a ku Beti-anati zinawasonkhera.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 1

Onani Oweruza 1:33 nkhani