Miyendo yace ikunga zoimiritsa za mwala wonyezimira,Zogwirika m'kamwa mwa golidi:Maonekedwe ace akunga Lebano, okometsetsa ngati mikungudza.