Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nyimbo 3:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Turukani, ana akazi inu a Ziyoni, mupenye Solomo mfumu,Ndi korona amace anambveka naye tsiku la ukwati wace,Ngakhale tsiku lakukondwera mtima wace.

Werengani mutu wathunthu Nyimbo 3

Onani Nyimbo 3:11 nkhani