Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nyimbo 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nkhunda yangawe, yokhala m'ming'alu ya thanthwe, mobisika motsetsereka,Ndipenye nkhope yako, ndimve manako;Pakuti mau ako ngokoma, nkhope yako ndi kukongola.

Werengani mutu wathunthu Nyimbo 2

Onani Nyimbo 2:14 nkhani