Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 9:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mlendo akakhala mwa inu, nakacitira Yehova Paskha, azicita monga mwa lemba la Paskha, ndi monga mwa ciweruzo cace; lemba likhale limodzi kwa inu, ndi kwa mlendo, ndi kwa wobadwa m'dziko.

Werengani mutu wathunthu Numeri 9

Onani Numeri 9:14 nkhani