Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 9:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akakhala woyera, wosakhala paulendo, koma akaleka kucita Paskha, amsadze munthuyo kwa anthu a mtundu wace; popeza sanabwera naco copereka ca Yehova pa nyengo yace yoikidwa, munthuyu asenze kucimwa kwace.

Werengani mutu wathunthu Numeri 9

Onani Numeri 9:13 nkhani