Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 8:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mapangidwe ace a coikapo nyali ndiwo golidi wosula; kuyambira tsinde lace kufikira maluwa ace anacisula; monga mwa maonekedwe ace Yehova anaonetsa Mose, momwemo anacipanga coikapo nyali.

Werengani mutu wathunthu Numeri 8

Onani Numeri 8:4 nkhani