Ndipo polowa Mose ku cihema cokomanako, kunena ndi iye, anamva Mau akunena naye ocokera ku cotetezerapo ciri pa likasa la mboni, ocokera pakati pa akerubi awiriwo; ndipo iye ananena naye.