Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 7:88 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi ng'ombe zonse za nsembe yoyamika ndizo ng'ombe makumi awiri ndi zinai, nkhosa zamphongo makumi asanu ndi limodzi, atonde makumi asanu ndi limodzi, ana a nkhosa a caka cimodzi makumi asanu ndi limodzi. Uku ndi kupereka ciperekere, litadzozedwa guwa la nsembe.

Werengani mutu wathunthu Numeri 7

Onani Numeri 7:88 nkhani