Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 5:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wansembe amlumbiritse, nanene kwa mkazi, Ngati sanagona nawe munthu mmodzi yense, ngati sunapatukira kucidetso, pokhala ndiwe wa mwamuna wako, upulumuke ku madzi owawa awa akudzetsa temberero.

Werengani mutu wathunthu Numeri 5

Onani Numeri 5:19 nkhani