Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 5:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo wansembeyo aike mkaziyo pamaso pa Mulungu, nabvula mutu wa mkaziyo, naike nsembe yaufa yacikumbutso m'manja mwace, ndiyo nsembe yaufa yansanje; ndipo m'manja mwace mwa wansembe muzikhala madzi owawa akudzetsa temberero.

Werengani mutu wathunthu Numeri 5

Onani Numeri 5:18 nkhani