Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 4:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atatha Aroni ndi ana ace amuna kuphimba malo opatulika, ndi zipangizo zace zonse za malo opatulika, pofuna kumuka am'cigono; atatero, ana a Kohati adze kuzinyamula; koma asakhudze zopatulikazo, kuti angafe. Zinthu izi ndizo akatundu a ana a Kohati m'cihema cokomanako.

Werengani mutu wathunthu Numeri 4

Onani Numeri 4:15 nkhani