Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 4:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Naikepo zipangizo zace zonse, zimene atumikira nazo pamenepo, mbale za zofukiza, mitungo, ndi zaolera, ndi mbale zowazira, zipangizo zonse za guwa la nsembe; nayalepo cophimba ca zikopa za akatumbu, ndi kupisako mphiko zace.

Werengani mutu wathunthu Numeri 4

Onani Numeri 4:14 nkhani