Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 36:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mwana wamkazi yense wa mapfuko a ana a Israyeli, wakukhala naco colowa, akwatibwe ndi wina wa banja la pfuko la kholo lace, kuti ana a Israyeli akhale naco yense colowa ca makolo ace.

Werengani mutu wathunthu Numeri 36

Onani Numeri 36:8 nkhani