Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 35:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo musamaipsa dziko muli m'mwemo; popeza mwazi uipsa dziko; pakuti kulibe kutetezera dziko cifukwa ca mwazi anaukhetsa m'mwemo, koma ndi mwazi wa iye anaukhetsa ndiwo.

Werengani mutu wathunthu Numeri 35

Onani Numeri 35:33 nkhani