Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 34:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

dera lanu la kumwela lidzakhala locokera ku cipululu ca Zini, kutsata m'mphepete mwa Edomu, ndi malire anu a kumwela adzakhala ocokera ku malekezero a Nyanja ya Mcere kum'mawa;

Werengani mutu wathunthu Numeri 34

Onani Numeri 34:3 nkhani