Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 34:23-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. Wa ana a Yosefe; wa pfuko la ana a Manase, kalonga Haniyeli mwana wa Efodi.

24. Wa pfuko la ana a Efraimu, kalonga Kemuyeli mwana wa Sipitana.

25. Wa pfuko la ana a Zebuloni, kalonga Elisafana mwana wa Paranaki.

26. Wa pfuko la ana a Isakara, kalonga Palitiyeli mwana wa Azana.

Werengani mutu wathunthu Numeri 34