Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 34:21-24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. Wa pfuko la Benjamini, Elidadi mwana wa Kisiloni.

22. Wa pfuko la ana a Dani, kalonga Buki mwana wa Yogili.

23. Wa ana a Yosefe; wa pfuko la ana a Manase, kalonga Haniyeli mwana wa Efodi.

24. Wa pfuko la ana a Efraimu, kalonga Kemuyeli mwana wa Sipitana.

Werengani mutu wathunthu Numeri 34