Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 34:18-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. Muwatengenso akalonga, kalonga mmodzi ku pfuko limodzi, agawe dziko likhale colowa cao.

19. Maina a amunawo ndiwo: wa pfuko la Yuda, Kalebi mwana wa Yefune.

20. Wa pfuko la ana a Simeoni, Semuyeli mwana wa Amihudi.

Werengani mutu wathunthu Numeri 34