Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 32:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu adakwerawo kuturuka m'Aigupto, kuyambira wa zaka makumi awiri ndi mphambu sadzaona dziko limene ndinalumbirira Abrahamu, ndi Isake, ndi Yakobo; popeza sananditsata Ine ndi mtima wonse;

Werengani mutu wathunthu Numeri 32

Onani Numeri 32:11 nkhani