Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 31:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ku gawo la ana a Israyeli utenge munthu mmodzi mwa anthu makumi asanu, mwa ng'ombe, mwa aburu, mwa nkhosa ndi mbuzi, mwa zoweta zonse, momwemo; nuzipereke kwa Alevi, akusunga udikiro wa kacisi wa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Numeri 31

Onani Numeri 31:30 nkhani