Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 27:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atate wathu adamwalira m'cipululu, ndipo sanakhala iye pakati pa msonkhano wa iwo akusonkhana kutsutsana ndi Yehova, mu msonkhano wa Kora; koma anafera zoipa zace zace; ndipo analibe ana amuna.

Werengani mutu wathunthu Numeri 27

Onani Numeri 27:3 nkhani