Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 26:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Tselofekadi mwana wa Heferi analibe ana amuna, koma ana akazi ndiwo; ndipo maina a ana akazi a Tselofekadi ndiwo Mala ndi Nowa, Hogila, Milika ndi Tiriza.

Werengani mutu wathunthu Numeri 26

Onani Numeri 26:33 nkhani