Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 24:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mulungu amturutsa m'Aigupto;Ali nayo mphamvu yonga ya njati;Adzawadya amitundu, ndiwo adani ace.Nadzaphwanya mafupa ao, Ndi kuwapyoza ndi mibvi yace.

Werengani mutu wathunthu Numeri 24

Onani Numeri 24:8 nkhani