Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 22:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Taonani, ndafika kwa inu; ngati ndiri nayo mphamvu konse tsopano kunena kanthu? mau amene Mulungu aike m'kamwa mwanga ndiwo ndidzanena.

Werengani mutu wathunthu Numeri 22

Onani Numeri 22:38 nkhani