Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 21:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Mose, Usamuopa; popeza ndampereka m'manja mwako, iye ndi anthu ace onse, ndi dziko lace; umcitire monga umo unacitira Sihoni mfumu ya Aamori anakhalayo ku Hesiboni.

Werengani mutu wathunthu Numeri 21

Onani Numeri 21:34 nkhani