Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 2:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo khamu la Alevi azimuka naco cihema cokomanako, pakati pa makamu; monga amamanga mahema ao, momwemo azimuka ulendo wao, munthu yense pamalo pace, monga mwa mbendera zao.

Werengani mutu wathunthu Numeri 2

Onani Numeri 2:17 nkhani