Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 19:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma munthu wakukhala wodetsedwa, koma wosadziyeretsa, azimsadza munthuyo pakati pa msonkhano, popeza waipsa malo opatulika a Yehova; sanamwaza madzi akusiyanitsa; ndiye wodetsedwa.

Werengani mutu wathunthu Numeri 19

Onani Numeri 19:20 nkhani