Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 18:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwe ndi ana ako amuna pamodzi ndi iwe mucite nchito yanu ya nsembe, pa zonse za ku guwa la nsembe, ndi za m'kati mwa nsaru yocinga; ndipo mutumikire; ndikupatsani nchito yanu ya nsembe, utumiki wopatsika kwaulere; koma mlendo wakuyandikiza amuphe.

Werengani mutu wathunthu Numeri 18

Onani Numeri 18:7 nkhani