Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 18:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ine, taonani, ndinatenga abale anu Alevi kuwacotsa pakati pa ana a Israyeli; ndiwo mphatso yanu, yopatsidwa kwa Yehova, kucita nchito ya cihema cokomanako.

Werengani mutu wathunthu Numeri 18

Onani Numeri 18:6 nkhani