Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 18:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mafuta onse okometsetsa, ndi vinyo watsopano, ndi tirigu yense wokometsetsa, zipatso zao zoyamba zimene aziperekako kwa Yehova, ndazipereka kwa iwe.

Werengani mutu wathunthu Numeri 18

Onani Numeri 18:12 nkhani