Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 18:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zako ndi izinso: nsembe yokweza ya mphatso yao, ndi nsembe zoweyula zonse za ana a Israyeli; ndazipereka kwa iwe, ndi kwa ana ako amuna ndi kwa ana ako akazi pamodzi ndi iwe, likhale lemba losatha; oyera onse a m'banja lako adyeko.

Werengani mutu wathunthu Numeri 18

Onani Numeri 18:11 nkhani