Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 17:11-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Ndipo Mose anacita monga Yehova adamuuza, momwemo anacita.

12. Pamenepo ana a Israyeli ananena ndi Mose, nati, Taonani, tikufa, tionongeka, tionongeka tonse.

13. Yense wakuyandikiza kacisi wa Yehova amwalira; kodi tidzatha nkufa?

Werengani mutu wathunthu Numeri 17