Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 17:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Mose, Bweza ndodo ya Aroni kulika cakuno ca mboni, isungike ikhale cizindikilo ca pa ana opikisana; kuti unelitsirizire madandaulo ao, kuti ungafe.

Werengani mutu wathunthu Numeri 17

Onani Numeri 17:10 nkhani