Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 15:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo cikhale kwa inu mphonje, yakuti muziyang'anirako, ndi kukumbukila malamulo onse a Yehova, ndi kuwacita, ndi kuti musamazondazonda kutsata za m'mtima mwanu, ndi za m'maso mwanu zimene mumatsata ndi cigololo;

Werengani mutu wathunthu Numeri 15

Onani Numeri 15:39 nkhani