Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 15:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza ananyoza mau a Yehova, nathyola lamulo lace; munthuyu amsadze konse; mphulupulu yace ikhale pa iye.

Werengani mutu wathunthu Numeri 15

Onani Numeri 15:31 nkhani