Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 13:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Udzitumire amuna, kuti azonde dziko la Kanani, limene ndirikupatsa ana a Israyeli; utumize munthu mmodzi wa pfuko liri lonse la makolo ao, yense kalonga pakati pa anzace.

Werengani mutu wathunthu Numeri 13

Onani Numeri 13:2 nkhani