Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 11:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo unene ndi anthu, Mudzipatuliretu, mawa mudzadya nyama; popeza mwalira m'makutu a Yehova, ndi kuti, Adzatipatsa nyama ndani? popeza tinakhala bwino m'Aigupto, Potero Yehova adzakupatsani nyama, ndipo mudzadya.

Werengani mutu wathunthu Numeri 11

Onani Numeri 11:18 nkhani