Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 9:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsono, Mulungu wathu, ndinu Mulungu wamkuru, ndi wamphamvu, ndi woopsa, wakusunga pangano ndi cifundo, asacepe pamaso panu mabvuto athu onse amene anatigwera ife, ndi mafumu athu, akuru athu, ndi ansembe athu, ndi aneneri athu, ndi makolo athu, ndi anthu anu onse, kuyambira masiku a mafumu a Asuri, mpaka lero lino.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:32 nkhani