Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 9:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo analanda midzi yamalinga, ndi dziko la zonona, nalandira zikhale zao zao nyumba zodza la ndi zokoma ziri zonse, zitsime zokumbidwa, minda yampesa, ndi minda yaazitona, ndi mitengo yambiri yazipatso; nadya iwo, nakhuta, nanenepa, nakondwera nako kukoma kwanu kwakukuru.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:25 nkhani